Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 23:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mfumuyo inaimirira pafupi ndi chipilala+ ndipo inachita pangano+ pamaso pa Yehova, kuti adzatsatira+ Yehova ndi kusunga malamulo ake+ ndi maumboni* ake.+ Adzachita zimenezi ndi mtima wonse+ ndi moyo wonse,+ mwa kutsatira mawu a pangano olembedwa m’bukulo.+ Choncho anthu onsewo anavomereza panganolo.+

  • 2 Mbiri 15:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kuwonjezera apo, anachita pangano+ loti adzafunafuna Yehova Mulungu wa makolo awo ndi mtima wawo wonse ndi moyo wawo wonse.+

  • 2 Mbiri 34:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Mfumuyo inaimirirabe pamalo ake+ ndipo inachita pangano+ pamaso pa Yehova, kuti idzatsatira Yehova ndi kusunga malamulo+ ake ndi maumboni*+ ake. Inanenanso kuti idzachita+ zimenezi ndi mtima wake wonse+ ndi moyo wake wonse,+ mogwirizana ndi mawu a pangano olembedwa m’bukulo.+

  • Ezara 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano tiyeni tichite pangano+ ndi Mulungu wathu, lakuti tisiya+ akazi onse amenewa ndi ana awo mogwirizana ndi lamulo la Yehova ndi la anthu amene akunjenjemera+ chifukwa cha lamulo+ la Mulungu wathu, kuti zinthu zichitike mogwirizana ndi lamulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena