1 Mafumu 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ana awo amene anatsala m’dzikomo, amene ana a Isiraeli analephera kuwawononga,+ Solomo anali kuwagwiritsa ntchito yaukapolo. Anthuwa akupitiriza kugwira ntchito yotere kufikira lero.+ Nehemiya 7:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ana a atumiki a Solomo:+ Ana a Sotai, ana a Sofereti, ana a Perida,*+
21 ana awo amene anatsala m’dzikomo, amene ana a Isiraeli analephera kuwawononga,+ Solomo anali kuwagwiritsa ntchito yaukapolo. Anthuwa akupitiriza kugwira ntchito yotere kufikira lero.+