2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo utenge ndodo+ ya fuko lililonse kwa mtsogoleri+ wa fukolo. Zikhalepo ndodo 12. Pandodo iliyonse ulembepo dzina la mtsogoleri wa fukolo.
12 Tsopano Davide anawauza kuti: “Inuyo ndinu atsogoleri+ a nyumba ya makolo a Alevi. Choncho inu ndi abale anu mudziyeretse,+ ndipo mukatenge likasa la Yehova Mulungu wa Isiraeli n’kukaliika kumalo amene ine ndakonza kuti likakhaleko.