Yoswa 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno atsogoleriwo anawauza kuti: “Akhale ndi moyo, ndipo akhale otola nkhuni ndi otungira madzi khamu lonse la Isiraeli,+ monga mmene tinawalonjezera.”+ Ezara 2:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Anetini+ onse pamodzi ndi ana a atumiki a Solomo analipo 392.+
21 Ndiyeno atsogoleriwo anawauza kuti: “Akhale ndi moyo, ndipo akhale otola nkhuni ndi otungira madzi khamu lonse la Isiraeli,+ monga mmene tinawalonjezera.”+