9 Kuwonjezera apo Uziya anamanga nsanja+ ku Yerusalemu pafupi ndi Chipata cha Pakona,+ Chipata cha Kuchigwa,+ ndiponso pafupi ndi Mchirikizo wa Khoma, ndipo nsanjazo anazilimbitsa.
13 Hanuni ndi anthu okhala ku Zanowa+ anakonza Chipata cha Kuchigwa.+ Iwo anachimanga ndi kuika zitseko zake,+ akapichi ake+ ndi mipiringidzo yake.+ Iwo anakonzanso mpandawo mikono* 1,000 mpaka kukafika ku Chipata cha Milu ya Phulusa.+