Yoswa 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Zanowa,+ Eni-ganimu, Tapuwa, Enamu, Nehemiya 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Hanuni ndi anthu okhala ku Zanowa+ anakonza Chipata cha Kuchigwa.+ Iwo anachimanga ndi kuika zitseko zake,+ akapichi ake+ ndi mipiringidzo yake.+ Iwo anakonzanso mpandawo mikono* 1,000 mpaka kukafika ku Chipata cha Milu ya Phulusa.+
13 Hanuni ndi anthu okhala ku Zanowa+ anakonza Chipata cha Kuchigwa.+ Iwo anachimanga ndi kuika zitseko zake,+ akapichi ake+ ndi mipiringidzo yake.+ Iwo anakonzanso mpandawo mikono* 1,000 mpaka kukafika ku Chipata cha Milu ya Phulusa.+