1 Mbiri 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Elipaala anali Ebere, Misamu, ndi Semedi. Semedi ndiye anamanga mzinda wa Ono+ ndiponso mzinda wa Lodi,+ ndi midzi yake yozungulira.
12 Ana a Elipaala anali Ebere, Misamu, ndi Semedi. Semedi ndiye anamanga mzinda wa Ono+ ndiponso mzinda wa Lodi,+ ndi midzi yake yozungulira.