Nehemiya 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Gulu lina loimba nyimbo zoyamika+ Mulungu linali kuyenda patsogolo, ndipo ine ndinali pambuyo pawo pamodzi ndi hafu ya anthuwo. Oimbawo anayenda pampandawo, kudutsa pamwamba pa Nsanja ya Mauvuni+ mpaka kukafika ku Khoma Lalikulu.+ Nehemiya 12:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Kenako magulu awiri oimba nyimbo zoyamikawo+ anafika panyumba+ ya Mulungu woona. Ine pamodzi ndi atsogoleri amene ndinali nawo tinafikanso komweko.+
38 Gulu lina loimba nyimbo zoyamika+ Mulungu linali kuyenda patsogolo, ndipo ine ndinali pambuyo pawo pamodzi ndi hafu ya anthuwo. Oimbawo anayenda pampandawo, kudutsa pamwamba pa Nsanja ya Mauvuni+ mpaka kukafika ku Khoma Lalikulu.+
40 Kenako magulu awiri oimba nyimbo zoyamikawo+ anafika panyumba+ ya Mulungu woona. Ine pamodzi ndi atsogoleri amene ndinali nawo tinafikanso komweko.+