Ezara 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Koresi mfumu ya Perisiya wanena kuti,+ ‘Yehova Mulungu wakumwamba+ wandipatsa+ maufumu onse a padziko lapansi. Iye wandituma kuti ndim’mangire nyumba ku Yerusalemu+ m’dziko la Yuda. Ezara 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwo anali atamaliza kumanga nyumbayo pofika tsiku lachitatu la mwezi wa Adara,+ m’chaka cha 6 cha ulamuliro wa mfumu Dariyo.
2 “Koresi mfumu ya Perisiya wanena kuti,+ ‘Yehova Mulungu wakumwamba+ wandipatsa+ maufumu onse a padziko lapansi. Iye wandituma kuti ndim’mangire nyumba ku Yerusalemu+ m’dziko la Yuda.
15 Iwo anali atamaliza kumanga nyumbayo pofika tsiku lachitatu la mwezi wa Adara,+ m’chaka cha 6 cha ulamuliro wa mfumu Dariyo.