Nehemiya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ndinauza mfumu kuti: “Ngati zili bwino ndi inu mfumu,+ ndipo ngati ine mtumiki wanu mungandikomere mtima,+ munditumize ku Yuda, kumzinda umene makolo anga anaikidwako kuti ndikaumangenso.”+ Nehemiya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mfumu inandiyankha kuti: “Ulendo wako udzatenga masiku angati, ndipo udzabwera liti?” Pa nthawiyi, mkazi wamkulu wa mfumu anali atakhala pambali pake. Choncho mfumu inandilola kupita nditaiuza nthawi.+
5 Kenako ndinauza mfumu kuti: “Ngati zili bwino ndi inu mfumu,+ ndipo ngati ine mtumiki wanu mungandikomere mtima,+ munditumize ku Yuda, kumzinda umene makolo anga anaikidwako kuti ndikaumangenso.”+
6 Mfumu inandiyankha kuti: “Ulendo wako udzatenga masiku angati, ndipo udzabwera liti?” Pa nthawiyi, mkazi wamkulu wa mfumu anali atakhala pambali pake. Choncho mfumu inandilola kupita nditaiuza nthawi.+