Esitere 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mfumu itangoona Mfumukazi Esitere itaima m’bwalo la nyumba ya mfumu, inamukomera mtima+ moti inamuloza ndi ndodo yachifumu ya golide+ imene inali m’manja mwake. Pamenepo Esitere anayandikira ndi kugwira pamwamba pa ndodoyo. Esitere 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno mfumu inaloza Esitere ndi ndodo yachifumu ya golide.+ Zitatero, Esitere anadzuka ndi kuima pamaso pa mfumu.
2 Mfumu itangoona Mfumukazi Esitere itaima m’bwalo la nyumba ya mfumu, inamukomera mtima+ moti inamuloza ndi ndodo yachifumu ya golide+ imene inali m’manja mwake. Pamenepo Esitere anayandikira ndi kugwira pamwamba pa ndodoyo.
4 Ndiyeno mfumu inaloza Esitere ndi ndodo yachifumu ya golide.+ Zitatero, Esitere anadzuka ndi kuima pamaso pa mfumu.