Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno anatumiza makalatawo kudzera mwa amtokoma+ kupita kuzigawo zonse za mfumu. Anachita izi kuti pa tsiku limodzi,+ pa tsiku la 13 la mwezi wa 12 umene ndi mwezi wa Adara,+ awononge, aphe ndi kufafaniza Ayuda onse, mnyamata komanso mwamuna wachikulire, ana ndi akazi ndi kufunkha zinthu zawo.+

  • Esitere 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 ana aamuna 10+ a Hamani+ mwana wa Hamedata amene anali kudana ndi Ayuda.+ Ayuda anapha amuna amenewa koma sanafunkhe+ zinthu zawo.

  • Esitere 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno Ayuda amene anali ku Susani anasonkhananso pamodzi pa tsiku la 14+ la mwezi wa Adara, ndipo anapha amuna 300 ku Susani, koma sanafunkhe zinthu zawo.+

  • Esitere 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ayuda ena onse amene anali m’zigawo+ za mfumu anasonkhana pamodzi kuti ateteze miyoyo yawo.+ Ndipo anabwezera+ adani awo ndi kupha anthu 75,000 amene anali kudana nawo, koma sanafunkhe zinthu zawo

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena