Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ngati zingakukomereni mfumu, palembedwe makalata kuti anthu amenewa awonongedwe. Ine ndidzapereka matalente 10,000+ asiliva kwa anthu amene adzagwira ntchito imeneyi+ kuti abweretse matalentewo mosungiramo chuma cha mfumu.”

  • Esitere 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano Esitere anati: “Ngati zingakukomereni mfumu, ndipo ngati mungandikomere mtima,+ komanso ngati n’zoyenera kwa inu mfumu ndiponso ngati ndine munthu wabwino kwa inu, palembedwe makalata ofafaniza makalata+ achiwembu amene Hamani, mwana wa Hamedata Mwagagi,+ analemba pofuna kuwononga Ayuda+ amene ali m’zigawo zanu zonse mfumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena