-
Danieli 6:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kenako anapita kwa mfumu ndi kuifunsa za lamulo limene inakhazikitsa lija, kuti: “Kodi inu mfumu, si paja mwakhazikitsa lamulo lonena kuti kwa masiku 30 munthu aliyense wopezeka akupemphera kwa mulungu kapena kwa munthu wina aliyense, kupatulapo kwa inu nokha, aponyedwe m’dzenje la mikango?”+ Mfumuyo inayankha kuti: “Nkhani imeneyi ndi yodziwika bwino, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya, amene sasintha.”+
-