Esitere 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo mfumu inavula mphete yodindira+ kudzanja lake ndi kuipereka kwa Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ amene anali kudana kwambiri ndi Ayuda.+ Esitere 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ana aamuna 10+ a Hamani+ mwana wa Hamedata amene anali kudana ndi Ayuda.+ Ayuda anapha amuna amenewa koma sanafunkhe+ zinthu zawo.
10 Pamenepo mfumu inavula mphete yodindira+ kudzanja lake ndi kuipereka kwa Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ amene anali kudana kwambiri ndi Ayuda.+
10 ana aamuna 10+ a Hamani+ mwana wa Hamedata amene anali kudana ndi Ayuda.+ Ayuda anapha amuna amenewa koma sanafunkhe+ zinthu zawo.