Esitere 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando+ akalonga ndi atumiki ake onse, akuluakulu a asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka+ ndi akalonga a m’zigawo za ufumu wake.+ Danieli 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamapeto pake, amuna amphamvu amenewa anapita kwa mfumu ali chigulu ndipo anaiuza kuti: “Inu mfumu, mukudziwa kuti malamulo a Amedi ndi Aperisiya amanena kuti lamulo lililonse+ lokhazikitsidwa ndi mfumu siliyenera kusinthidwa.”+
3 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando+ akalonga ndi atumiki ake onse, akuluakulu a asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka+ ndi akalonga a m’zigawo za ufumu wake.+
15 Pamapeto pake, amuna amphamvu amenewa anapita kwa mfumu ali chigulu ndipo anaiuza kuti: “Inu mfumu, mukudziwa kuti malamulo a Amedi ndi Aperisiya amanena kuti lamulo lililonse+ lokhazikitsidwa ndi mfumu siliyenera kusinthidwa.”+