Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiye inu lembani makalata m’malo mwa Ayuda. Mulembe zimene mukuona kuti n’zabwino kwa inu m’dzina la mfumu.+ Mudinde makalatawo ndi mphete yodindira ya mfumu, pakuti n’zosatheka kufafaniza makalata amene alembedwa m’dzina la mfumu ndi kudindidwa ndi mphete yake yodindira.”+

  • Salimo 94:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kodi inu mudzagwirizana ndi olamulira ankhanza,+

      Pamene akuyambitsa mavuto mwa kupanga malamulo?+

  • Danieli 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsopano inu mfumu khazikitsani lamulo ndipo musaine+ kuti lamulolo lisasinthe, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya,+ amene sasintha.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena