1 Petulo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo kudzikongoletsa kwanu kusakhale kwakunja, monga kumanga tsitsi,+ kuvala zodzikongoletsera zagolide,+ kapena kuvala malaya ovala pamwamba.
3 Ndipo kudzikongoletsa kwanu kusakhale kwakunja, monga kumanga tsitsi,+ kuvala zodzikongoletsera zagolide,+ kapena kuvala malaya ovala pamwamba.