Esitere 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’bukumo anapeza kuti mwalembedwa zimene Moredekai anaulula+ zokhudza Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri+ za panyumba ya mfumu, alonda apakhomo, amene anafuna kupha Mfumu Ahasiwero.
2 M’bukumo anapeza kuti mwalembedwa zimene Moredekai anaulula+ zokhudza Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri+ za panyumba ya mfumu, alonda apakhomo, amene anafuna kupha Mfumu Ahasiwero.