Yobu 38:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kodi madzi oundana amachokera m’mimba mwa ndani,Ndipo mame oundana+ a m’mlengalenga anawabereka ndani? Salimo 147:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye amapereka chipale chofewa kuti chikhale ngati ubweya wa nkhosa.+Amamwaza mame oundana ngati kuti ndi phulusa.+
29 Kodi madzi oundana amachokera m’mimba mwa ndani,Ndipo mame oundana+ a m’mlengalenga anawabereka ndani?
16 Iye amapereka chipale chofewa kuti chikhale ngati ubweya wa nkhosa.+Amamwaza mame oundana ngati kuti ndi phulusa.+