Yobu 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa chipale chofewa amachiuza kuti, ‘Gwera padziko lapansi.’+Amauzanso mvula zimenezi, ngakhalenso mvula yamphamvu ikamakhuthuka.+ Salimo 148:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu moto ndi matalala, chipale chofewa ndi utsi wakuda bii,+Iwe mphepo yamkuntho yokwaniritsa mawu ake.+
6 Chifukwa chipale chofewa amachiuza kuti, ‘Gwera padziko lapansi.’+Amauzanso mvula zimenezi, ngakhalenso mvula yamphamvu ikamakhuthuka.+
8 Inu moto ndi matalala, chipale chofewa ndi utsi wakuda bii,+Iwe mphepo yamkuntho yokwaniritsa mawu ake.+