Yobu 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anakulunga madzi m’mitambo yake,+Moti mitamboyo sing’ambika pansi pa madziwo. Yobu 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuti mphepo aipatse mphamvu.+Ndipo iye amagawa madzi ndi choyezera.+ Yobu 38:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Madzi amadzibisa ngati kuti ali pansi pa mwala,Ndipo pamwamba pa madzi akuya pamauma.+ Mabuku a Chichewa (1974-2025) Tulukani Lowani Chichewa Tumizirani Ena Zimene Mumakonda Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Zoyenera Kutsatira Nkhani Yosunga Chinsinsi Privacy Settings JW.ORG Lowani Tumizirani Ena Tumizirani Wina pa Imelo
8 Iye anakulunga madzi m’mitambo yake,+Moti mitamboyo sing’ambika pansi pa madziwo. Yobu 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuti mphepo aipatse mphamvu.+Ndipo iye amagawa madzi ndi choyezera.+ Yobu 38:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Madzi amadzibisa ngati kuti ali pansi pa mwala,Ndipo pamwamba pa madzi akuya pamauma.+
25 Kuti mphepo aipatse mphamvu.+Ndipo iye amagawa madzi ndi choyezera.+ Yobu 38:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Madzi amadzibisa ngati kuti ali pansi pa mwala,Ndipo pamwamba pa madzi akuya pamauma.+