-
Salimo 135:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Amachititsa nthunzi kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+
Iye anapanganso zipata zotulukirapo mvula.+
Amachititsa mphepo kutuluka m’nkhokwe zake.+
-
Salimo 148:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Inu moto ndi matalala, chipale chofewa ndi utsi wakuda bii,+
Iwe mphepo yamkuntho yokwaniritsa mawu ake.+
-
-
-