Genesis 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma nkhungu+ inali kukwera m’mwamba kuchokera padziko lapansi, ndipo inali kunyowetsa nthaka yonse.+ Yeremiya 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mawu ake amapangitsa madzi akumwamba kuchita mkokomo,+ ndipo amachititsa nthunzi kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Iye wapanganso zipata zotulukirapo mvula+ ndipo amatulutsa mphepo yamkuntho m’nkhokwe zake.+ Yeremiya 51:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu ake amapangitsa madzi akumwamba kuchita mkokomo, ndipo amachititsa nthunzi kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Iye wapanganso zipata zotulukirapo mvula+ ndipo amatulutsa mphepo yamkuntho m’nkhokwe zake.
6 Koma nkhungu+ inali kukwera m’mwamba kuchokera padziko lapansi, ndipo inali kunyowetsa nthaka yonse.+
13 Mawu ake amapangitsa madzi akumwamba kuchita mkokomo,+ ndipo amachititsa nthunzi kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Iye wapanganso zipata zotulukirapo mvula+ ndipo amatulutsa mphepo yamkuntho m’nkhokwe zake.+
16 Mawu ake amapangitsa madzi akumwamba kuchita mkokomo, ndipo amachititsa nthunzi kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Iye wapanganso zipata zotulukirapo mvula+ ndipo amatulutsa mphepo yamkuntho m’nkhokwe zake.