Salimo 111:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ntchito za Yehova ndi zazikulu,+ד [Daʹleth]Onse amene amasangalala nazo amazisinkhasinkha.+ Salimo 145:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzasinkhasinkha za ulemerero wanu waukulu+Ndi nkhani zokhudza ntchito zanu zodabwitsa.+