Salimo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Onse okhala padziko lapansi aope Yehova.+Anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi achite naye mantha.+ Miyambo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha kudziwa zinthu.+ Nzeru ndi malangizo zimanyozedwa ndi zitsiru.*+ Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
8 Onse okhala padziko lapansi aope Yehova.+Anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi achite naye mantha.+
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+