Ekisodo 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Motero panagwa matalala, ndipo panali kuwalima moto. Panagwa matalala amphamvu kwambiri amene sanaonekepo n’kale lonse m’dziko lonse la Iguputo.+ Ezekieli 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzatumiza mphepo yamkuntho, mvula yambiri ndi matalala, kusonyeza mkwiyo wanga kuti ndikuwonongeni.+
24 Motero panagwa matalala, ndipo panali kuwalima moto. Panagwa matalala amphamvu kwambiri amene sanaonekepo n’kale lonse m’dziko lonse la Iguputo.+
13 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzatumiza mphepo yamkuntho, mvula yambiri ndi matalala, kusonyeza mkwiyo wanga kuti ndikuwonongeni.+