Luka 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfarisi uja anaimirira+ ndi kuyamba kupemphera+ mumtima mwake. Iye anati, ‘Mulungu wanga, ndikukuyamikani chifukwa ine sindili ngati anthu enawa ayi. Iwo ndi olanda, osalungama ndi achigololo. Sindilinso ngati wokhometsa msonkho uyu.+
11 Mfarisi uja anaimirira+ ndi kuyamba kupemphera+ mumtima mwake. Iye anati, ‘Mulungu wanga, ndikukuyamikani chifukwa ine sindili ngati anthu enawa ayi. Iwo ndi olanda, osalungama ndi achigololo. Sindilinso ngati wokhometsa msonkho uyu.+