Nehemiya 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano adani athuwo anamva kuti tadziwa za chiwembu chawo, mwakuti Mulungu woona anasokoneza cholinga chawo.+ Zitatero tonse tinabwerera ku ntchito yomanga mpanda, aliyense pa ntchito yake.
15 Tsopano adani athuwo anamva kuti tadziwa za chiwembu chawo, mwakuti Mulungu woona anasokoneza cholinga chawo.+ Zitatero tonse tinabwerera ku ntchito yomanga mpanda, aliyense pa ntchito yake.