Salimo 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu a mitundu ina agwera m’dzenje limene anakumba okha.+Phazi lawo lakodwa mu ukonde+ umene anatchera okha.+
15 Anthu a mitundu ina agwera m’dzenje limene anakumba okha.+Phazi lawo lakodwa mu ukonde+ umene anatchera okha.+