Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+ Yakobo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+
18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+
8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+