Miyambo 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mtima wa munthu ukhoza kupirira matenda,+ koma mtima wosweka ndani angaupirire?+