Yobu 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero, kodi chiyembekezo changa chili kuti?+Kodi pali amene akuona kuti ine ndili ndi chiyembekezo? Aroma 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Popeza chilengedwe chinaperekedwa ku mkhalidwe wopanda pake,+ osati mwa kufuna kwake koma kudzera mwa iye amene anachipereka, pa maziko a chiyembekezo+
15 Chotero, kodi chiyembekezo changa chili kuti?+Kodi pali amene akuona kuti ine ndili ndi chiyembekezo?
20 Popeza chilengedwe chinaperekedwa ku mkhalidwe wopanda pake,+ osati mwa kufuna kwake koma kudzera mwa iye amene anachipereka, pa maziko a chiyembekezo+