-
Yobu 14:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Madzi amaperesa ngakhale miyala.
Akamathamanga amakokolola dothi la padziko lapansi.
Inunso mwawononga chiyembekezo cha munthu.
-
-
Yobu 19:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Akundikokera pansi mbali zonse, ine n’kuchoka.
Wazula chiyembekezo changa ngati mtengo.
-