Yobu 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 N’chifukwa chiyani anthu ena amadikirira imfa, koma siwabwerera,+Ngakhale amakumba pansi poifunafuna, kuposa mmene amakumbira chuma chobisika? Chivumbulutso 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku amenewo, anthuwo adzafunafuna imfa,+ koma sadzaipeza. Adzalakalaka kufa, koma imfa izidzawathawa.
21 N’chifukwa chiyani anthu ena amadikirira imfa, koma siwabwerera,+Ngakhale amakumba pansi poifunafuna, kuposa mmene amakumbira chuma chobisika?
6 M’masiku amenewo, anthuwo adzafunafuna imfa,+ koma sadzaipeza. Adzalakalaka kufa, koma imfa izidzawathawa.