Salimo 107:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anayendayenda m’chipululu+ mopanda kanthu.+Sanapeze njira iliyonse yopita kumzinda woti azikhalamo.+ Salimo 107:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mulungu akutsanulira mnyozo pa anthu olemekezeka,+Moti iye akuwachititsa kuyendayenda m’chipululu, mmene mulibe njira.+
4 Iwo anayendayenda m’chipululu+ mopanda kanthu.+Sanapeze njira iliyonse yopita kumzinda woti azikhalamo.+
40 Mulungu akutsanulira mnyozo pa anthu olemekezeka,+Moti iye akuwachititsa kuyendayenda m’chipululu, mmene mulibe njira.+