1 Mafumu 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi wapha munthu+ n’kutenganso munda wake?”’+ Ukamuuzenso kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pamalo+ amene agalu ananyambita magazi a Naboti, pomweponso agalu adzanyambita magazi ako, a iweyo.”’”+ 2 Mafumu 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero iye anatengera Yehoyakini+ ku Babulo.+ Anatenga ku Yerusalemu mayi a mfumuyo,+ akazi ake, nduna za panyumba yake,+ ndi akuluakulu a m’dzikolo, n’kuwapititsa ku Babulo. 2 Mafumu 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+
19 Ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Kodi wapha munthu+ n’kutenganso munda wake?”’+ Ukamuuzenso kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pamalo+ amene agalu ananyambita magazi a Naboti, pomweponso agalu adzanyambita magazi ako, a iweyo.”’”+
15 Chotero iye anatengera Yehoyakini+ ku Babulo.+ Anatenga ku Yerusalemu mayi a mfumuyo,+ akazi ake, nduna za panyumba yake,+ ndi akuluakulu a m’dzikolo, n’kuwapititsa ku Babulo.
7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+