Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+ Yobu 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Aang’ono ndi aakulu amakhala chimodzimodzi kumeneko,+Ndipo kapolo amamasuka kwa mbuye wake. Mlaliki 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zonse zimapita kumalo amodzi.+ Zonse zinachokera kufumbi+ ndipo zonse zimabwerera kufumbi.+
19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+