Yobu 31:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Palibe mlendo amene ankagona panja usiku.+Zitseko zanga ndinkazisiya zotsegula kwa odutsa m’njira.
32 Palibe mlendo amene ankagona panja usiku.+Zitseko zanga ndinkazisiya zotsegula kwa odutsa m’njira.