Mateyu 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Odala ndi anthu achifundo,+ chifukwa adzachitiridwa chifundo. 1 Petulo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pomaliza, nonsenu mukhale amaganizo amodzi,+ omverana chisoni, okonda abale, achifundo chachikulu,+ ndiponso amaganizo odzichepetsa.+
8 Pomaliza, nonsenu mukhale amaganizo amodzi,+ omverana chisoni, okonda abale, achifundo chachikulu,+ ndiponso amaganizo odzichepetsa.+