Genesis 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Motero Mulungu analenga munthu m’chifaniziro chake,+ m’chifaniziro cha Mulungu anam’lenga iye. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+ Yobu 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tafunsa m’badwo wakale,+Ndipo ganizira zinthu zimene makolo awo anafufuza.+
27 Motero Mulungu analenga munthu m’chifaniziro chake,+ m’chifaniziro cha Mulungu anam’lenga iye. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+