Miyambo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zamtengo wapatali zidzakhala zopanda phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+ Mlaliki 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pali chinthu chomvetsa chisoni kwambiri chimene ndaona padziko lapansi pano: Munthu kumangosunga chuma chake n’kudzapwetekedwa nacho.+
4 Zinthu zamtengo wapatali zidzakhala zopanda phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+
13 Pali chinthu chomvetsa chisoni kwambiri chimene ndaona padziko lapansi pano: Munthu kumangosunga chuma chake n’kudzapwetekedwa nacho.+