Mlaliki 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wotumikira munthu wina amagona tulo tokoma+ ngakhale adye zochepa kapena zambiri. Koma zambiri zimene munthu wolemera amakhala nazo zimamulepheretsa kugona.
12 Wotumikira munthu wina amagona tulo tokoma+ ngakhale adye zochepa kapena zambiri. Koma zambiri zimene munthu wolemera amakhala nazo zimamulepheretsa kugona.