Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndidzagona pansi ndi kupeza tulo mu mtendere,+

      Pakuti inu nokha Yehova mumandichititsa kukhala wotetezeka.+

  • Miyambo 3:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Nthawi iliyonse ukagona sudzaopa chilichonse.+ Udzagona ndithu, ndipo tulo tako tidzakhala tokoma.+

  • Yeremiya 31:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pamenepo, ndinagalamuka ndi kuyamba kuona. Ndinali nditagona tulo tokoma.

  • Mateyu 6:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Pa chifukwa chimenechi, ndikukuuzani kuti: Lekani kudera nkhawa+ moyo wanu kuti mudzadya chiyani, kapena mudzamwa chiyani, kapenanso kuti mudzavala chiyani.+ Kodi moyo suposa chakudya, ndipo kodi thupi siliposa chovala?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena