Numeri 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nyamayo ikadali m’kamwa mwawo,+ asanaitafune, mkwiyo wa Yehova unawayakira+ anthuwo. Ndipo Yehova anayamba kuwakantha anthuwo n’kuwapha ambiri.+ Salimo 78:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nthawi yomweyo, mkwiyo wa Mulungu unatsikira pa iwo.+Iye anayamba kupha anthu awo amphamvu.+Ndipo anakomola anyamata a mu Isiraeli.
33 Nyamayo ikadali m’kamwa mwawo,+ asanaitafune, mkwiyo wa Yehova unawayakira+ anthuwo. Ndipo Yehova anayamba kuwakantha anthuwo n’kuwapha ambiri.+
31 Nthawi yomweyo, mkwiyo wa Mulungu unatsikira pa iwo.+Iye anayamba kupha anthu awo amphamvu.+Ndipo anakomola anyamata a mu Isiraeli.