Yobu 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gawo la munthu woipa lochokera kwa Mulungu,+Zomwe adzalandire kwa Wamphamvuyonse monga cholowa cha ozunza anzawo, ndi izi: Yobu 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi si paja wochita zoipa amakumana ndi zosautsa,+Ndipo ochitira anzawo zopweteka tsoka limawagwera? Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
13 Gawo la munthu woipa lochokera kwa Mulungu,+Zomwe adzalandire kwa Wamphamvuyonse monga cholowa cha ozunza anzawo, ndi izi:
3 Kodi si paja wochita zoipa amakumana ndi zosautsa,+Ndipo ochitira anzawo zopweteka tsoka limawagwera?
7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+