Salimo 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Patukani pa zinthu zoipa ndipo chitani zabwino.+Funafunani mtendere ndi kuusunga.+ 1 Atesalonika 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pewani zoipa zamtundu uliwonse.+