Salimo 73:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Haa! M’kanthawi kochepa, iwo akhala chinthu chodabwitsa.+Afika pamapeto awo ndipo atha chifukwa cha masoka owagwera modzidzimutsa! Luka 12:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 mbuye wa kapoloyo adzabwera pa tsiku limene iye sakuyembekezera, ndi pa ola limene sakulidziwa,+ ndipo adzam’patsa chilango choopsa ndi kum’patsa gawo pamodzi ndi anthu osakhulupirika.+
19 Haa! M’kanthawi kochepa, iwo akhala chinthu chodabwitsa.+Afika pamapeto awo ndipo atha chifukwa cha masoka owagwera modzidzimutsa!
46 mbuye wa kapoloyo adzabwera pa tsiku limene iye sakuyembekezera, ndi pa ola limene sakulidziwa,+ ndipo adzam’patsa chilango choopsa ndi kum’patsa gawo pamodzi ndi anthu osakhulupirika.+