Salimo 74:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu munavundula nyanja ndi mphamvu zanu.+Pakati pa madzi munadula mitu ya zilombo za m’nyanja.+ Yesaya 51:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Koma ine Yehova ndine Mulungu wako, amene ndimavundula nyanja kuti mafunde ake achite phokoso.+ Yehova wa makamu ndiye dzina langa.+
15 “Koma ine Yehova ndine Mulungu wako, amene ndimavundula nyanja kuti mafunde ake achite phokoso.+ Yehova wa makamu ndiye dzina langa.+