Yesaya 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi anthu inu mudzatani pa tsiku limene adzatembenukire kwa inu+ ndi kukubweretserani chiwonongeko chochokera kutali?+ Mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+ ndipo ulemerero wanu mudzausiya kuti?+ Amosi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+
3 Kodi anthu inu mudzatani pa tsiku limene adzatembenukire kwa inu+ ndi kukubweretserani chiwonongeko chochokera kutali?+ Mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+ ndipo ulemerero wanu mudzausiya kuti?+
14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+